Mateyu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yesu anatembenuka, ndipo anaona mayiyo n’kunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+ Luka 8:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Mwanawe, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.+ Pita mu mtendere.”+ Aefeso 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwa kukoma mtima kwakukulu kumeneku, ndithudi mwapulumutsidwa kudzera m’chikhulupiriro,+ osati mwa inu nokha,+ koma monga mphatso ya Mulungu.+
22 Yesu anatembenuka, ndipo anaona mayiyo n’kunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+
8 Mwa kukoma mtima kwakukulu kumeneku, ndithudi mwapulumutsidwa kudzera m’chikhulupiriro,+ osati mwa inu nokha,+ koma monga mphatso ya Mulungu.+