Maliko 10:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Yesu anamuuza kuti: “Pita, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kutsatira Yesu mumsewu.+ Luka 7:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Chikhulupiriro chako chakupulumutsa.+ Pita mu mtendere.”+ Luka 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Yesu anauza munthuyo kuti: “Nyamuka uzipita. Chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Luka 18:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Choncho Yesu anamuuza kuti: “Yamba kuona, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Machitidwe 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwamuna ameneyu anali kumvetsera pamene Paulo anali kulankhula. Ndiyeno Paulo atamuyang’anitsitsa anaona kuti ali ndi chikhulupiriro+ ndipo angathe kuchiritsidwa.
52 Yesu anamuuza kuti: “Pita, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kutsatira Yesu mumsewu.+
9 Mwamuna ameneyu anali kumvetsera pamene Paulo anali kulankhula. Ndiyeno Paulo atamuyang’anitsitsa anaona kuti ali ndi chikhulupiriro+ ndipo angathe kuchiritsidwa.