Mateyu 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Atagwidwa ndi chifundo, Yesu anagwira maso awo.+ Nthawi yomweyo akhunguwo anayamba kuona ndipo anam’tsatira.+ Luka 7:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Chikhulupiriro chako chakupulumutsa.+ Pita mu mtendere.”+ Luka 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Yesu anauza munthuyo kuti: “Nyamuka uzipita. Chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+
34 Atagwidwa ndi chifundo, Yesu anagwira maso awo.+ Nthawi yomweyo akhunguwo anayamba kuona ndipo anam’tsatira.+