Ekisodo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni,+ chifukwa mwatinunkhitsa+ pamaso pa Farao ndi atumiki ake, moti mwawapatsa lupanga m’manja mwawo kuti atiphe.”+ 1 Samueli 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+ Salimo 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+
21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni,+ chifukwa mwatinunkhitsa+ pamaso pa Farao ndi atumiki ake, moti mwawapatsa lupanga m’manja mwawo kuti atiphe.”+
12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+
43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+