1 Samueli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova akhale mboni yathu mpaka kalekale,+ pa mawu awa amene tauzana+ ine ndi iwe.” 1 Samueli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova. Zitatero, Davide anapitiriza kukhala ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo. 2 Samueli 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndithu, ndikusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani bambo ako.+ Ndikubwezera munda wonse+ wa Sauli agogo ako ndipo iweyo uzidya mkate patebulo langa nthawi zonse.”+
18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova. Zitatero, Davide anapitiriza kukhala ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo.
7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndithu, ndikusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani bambo ako.+ Ndikubwezera munda wonse+ wa Sauli agogo ako ndipo iweyo uzidya mkate patebulo langa nthawi zonse.”+