Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 19:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pakuti kwa inu mbuyanga mfumu, nyumba yonse ya bambo anga ikanayenera kuwonongedwa, koma m’malomwake mwaika ine mtumiki wanu pakati pa anthu amene akudya chakudya patebulo+ la mfumu. Ndiye ndili ndi chifukwa chanji chomveka chopitirizira kudandaula+ kwa inu mfumu?”

  • 1 Mafumu 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Ana a Barizilai+ Mgiliyadi uwasonyeze kukoma mtima kosatha. Azikhala pakati pa anthu odyera nawe limodzi patebulo,+ chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinali kuthawa m’bale wako Abisalomu.+

  • Miyambo 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Munthu wopatsa mowolowa manja adzalandira mphoto,+ ndipo wothirira ena mosaumira nayenso adzathiriridwa mosaumira.+

  • Yesaya 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma munthu wopatsa amapereka malangizo okhudza kupatsa, ndipo iyeyo amapitiriza kukhala wopatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena