28 Pakuti kwa inu mbuyanga mfumu, nyumba yonse ya bambo anga ikanayenera kuwonongedwa, koma m’malomwake mwaika ine mtumiki wanu pakati pa anthu amene akudya chakudya patebulo+ la mfumu. Ndiye ndili ndi chifukwa chanji chomveka chopitirizira kudandaula+ kwa inu mfumu?”