Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense wotsala wa m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani.”+

  • 2 Samueli 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndithu, ndikusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani bambo ako.+ Ndikubwezera munda wonse+ wa Sauli agogo ako ndipo iweyo uzidya mkate patebulo langa nthawi zonse.”+

  • 2 Samueli 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iweyo, ana ako aamuna ndi antchito ako, muzimulimira munda wake ndi kumukololera kuti anthu a m’nyumba ya mdzukulu wa mbuye wako azikhala ndi chakudya chimene azidya. Koma Mefiboseti, mdzukulu wa mbuye wako, azidya chakudya patebulo langa nthawi zonse.”+

      Tsopano Ziba anali ndi ana aamuna 15 ndi antchito 20.+

  • 2 Samueli 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho Mefiboseti anali kukhala mu Yerusalemu pakuti anali kudya patebulo la mfumu nthawi zonse.+ Iye anali wolumala mapazi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena