-
1 Samueli 22:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Pakuti nonsenu mwandikonzera chiwembu chifukwa palibe aliyense amene anaulula kwa ine+ pamene mwana wanga anachita pangano+ ndi mwana wa Jese. Palibenso aliyense wa inu amene wandimvera chifundo ndi kuulula kwa ine kuti mwana wanga weniweni wasandutsa mtumiki wanga kukhala wondibisalira kuti andichite chiwembu monga mmene zililimu.”
-