42 Pamenepo Yonatani anauza Davide kuti: “Pita mu mtendere,+ pakuti tonse awiri talumbira+ m’dzina la Yehova kuti, ‘Yehova akhale pakati pa iwe ndi ine, ndi pakati pa ana ako ndi ana anga mpaka kalekale.’”+
Chotero Davide ananyamuka ndi kupita, koma Yonatani anabwerera kumzinda.