Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+ 1 Samueli 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yonatani ndi Davide anachita pangano,+ chifukwa Yonatani anali kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera.+ 1 Samueli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova. Zitatero, Davide anapitiriza kukhala ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo.
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+
3 Yonatani ndi Davide anachita pangano,+ chifukwa Yonatani anali kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera.+
18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova. Zitatero, Davide anapitiriza kukhala ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo.