1 Samueli 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Sauli ananyamuka+ ndi kupita kuchipululu cha Zifi, pamodzi ndi amuna osankhidwa mwapadera 3,000+ a mu Isiraeli, kuti akafunefune Davide kuchipululuko. Salimo 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]
2 Pamenepo Sauli ananyamuka+ ndi kupita kuchipululu cha Zifi, pamodzi ndi amuna osankhidwa mwapadera 3,000+ a mu Isiraeli, kuti akafunefune Davide kuchipululuko.
3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]