1 Samueli 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akazungulirazungulira, anali kubwerera ku Rama,+ chifukwa kumeneko n’kumene kunali nyumba yake, ndipo anali kuweruza Isiraeli ali kumeneko. Komanso iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+ 1 Samueli 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Samueli anali atamwalira ndipo Aisiraeli anali atamulira ndi kumuika m’manda mumzinda wakwawo ku Rama.+ Ndipo Sauli anali atachotsa anthu olankhula ndi mizimu ndi akatswiri olosera zam’tsogolo m’dzikolo.+
17 Akazungulirazungulira, anali kubwerera ku Rama,+ chifukwa kumeneko n’kumene kunali nyumba yake, ndipo anali kuweruza Isiraeli ali kumeneko. Komanso iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+
3 Tsopano Samueli anali atamwalira ndipo Aisiraeli anali atamulira ndi kumuika m’manda mumzinda wakwawo ku Rama.+ Ndipo Sauli anali atachotsa anthu olankhula ndi mizimu ndi akatswiri olosera zam’tsogolo m’dzikolo.+