Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 19:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho anadutsa ndi kupitirizabe ulendo wawo ndipo dzuwa linayamba kulowa atayandikira Gibeya, m’dera la Benjamini.

  • 1 Samueli 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+

  • 1 Samueli 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mithengayo inafika ku Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, ndi kuuza anthu uthengawo. Anthu onse atamva uthengawo anayamba kulira mokweza mawu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena