Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+