Numeri 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ataona Akeni,+ anapitirizanso mawu ake a ndakatulo, kuti:“Mokhala mwanu ndi mokhazikika, malo okhala inu ali pathanthwe. 1 Samueli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zili choncho, Sauli anauza Akeni+ kuti: “Nyamukani,+ muchoke pakati pa Aamaleki kuti ndisakuwonongeni pamodzi nawo. Inuyo munasonyeza kukoma mtima kosatha kwa ana onse a Isiraeli+ atatuluka mu Iguputo.”+ Choncho Akeni anachokadi pakati pa Aamaleki.
21 Iye ataona Akeni,+ anapitirizanso mawu ake a ndakatulo, kuti:“Mokhala mwanu ndi mokhazikika, malo okhala inu ali pathanthwe.
6 Zili choncho, Sauli anauza Akeni+ kuti: “Nyamukani,+ muchoke pakati pa Aamaleki kuti ndisakuwonongeni pamodzi nawo. Inuyo munasonyeza kukoma mtima kosatha kwa ana onse a Isiraeli+ atatuluka mu Iguputo.”+ Choncho Akeni anachokadi pakati pa Aamaleki.