1 Samueli 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo Aheberi amene anali atagwirizana ndi Afilisiti+ poyamba, amene anali atapita kukakhala mumsasa wa Afilisiti, nawonso anakhala kumbali ya Aisiraeli amene anali ndi Sauli ndi Yonatani.
21 Ndipo Aheberi amene anali atagwirizana ndi Afilisiti+ poyamba, amene anali atapita kukakhala mumsasa wa Afilisiti, nawonso anakhala kumbali ya Aisiraeli amene anali ndi Sauli ndi Yonatani.