11 Zitatero, amuna 3,000 a ku Yuda anapita kuphanga la thanthwe la Etami+ ndi kuuza Samisoni kuti: “Kodi iwe, sukudziwa kuti Afilisiti ndi amene akutilamulira?+ Ndiye wachitiranji zimenezi kwa ife?” Iye anawayankha kuti: “Ndawachitira zimene iwo anandichitira.”+