Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+

  • Oweruza 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ana a Isiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ moti Yehova anawapereka m’manja mwa Afilisiti+ zaka 40.

  • Oweruza 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Bambo ndi mayi a Samisoni sanadziwe kuti Yehova ndi amene anali kuchititsa zimenezi.+ Iwo sanadziwe kuti anali kufunafuna mpata woti amenyane ndi Afilisiti, chifukwa pa nthawiyi Afilisiti anali kulamulira Isiraeli.+

  • Salimo 106:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+

      Kuti anthu odana nawo awalamulire,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena