Yoswa 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova analola mitunduyo kuumitsa mitima+ yawo kuti ichite nkhondo ndi Aisiraeli. Anatero kuti iye awawononge ndi kuti Aisiraeliwo asawamvere chisoni,+ koma kuti awatheretu monga mmene Yehova analamulira Mose.+ 1 Mafumu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo.
20 Yehova analola mitunduyo kuumitsa mitima+ yawo kuti ichite nkhondo ndi Aisiraeli. Anatero kuti iye awawononge ndi kuti Aisiraeliwo asawamvere chisoni,+ koma kuti awatheretu monga mmene Yehova analamulira Mose.+
15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo.