1 Samueli 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davide analanditsa zonse zimene Aamaleki anatenga,+ n’kulanditsanso akazi ake awiri aja. Salimo 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Masoka a munthu wolungama ndi ochuluka,+Koma Yehova amamupulumutsa ku masoka onsewo.+ Miyambo 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wolungama ndi amene amapulumutsidwa ku zowawa,+ ndipo woipa amalowa m’malo mwake.+ Miyambo 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 pakuti wolungama akhoza kugwa ngakhale nthawi 7 ndipo ndithu adzadzukanso.+ Koma anthu oipa, tsoka lidzawapunthwitsa.+
16 pakuti wolungama akhoza kugwa ngakhale nthawi 7 ndipo ndithu adzadzukanso.+ Koma anthu oipa, tsoka lidzawapunthwitsa.+