Deuteronomo 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Kapolo akathawira kwa iwe kuchokera kwa mbuye wake, usam’bweze kwa mbuye wakeyo.+ Deuteronomo 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Apitirize kukhala ndi iwe pakati panu, pamalo alionse amene iye angasankhe mu umodzi mwa mizinda yanu,+ kulikonse kumene wakonda. Usamamuzunze.+
16 Apitirize kukhala ndi iwe pakati panu, pamalo alionse amene iye angasankhe mu umodzi mwa mizinda yanu,+ kulikonse kumene wakonda. Usamamuzunze.+