Yesaya 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu inu, perekani malangizo. Chitani zimene zagamulidwa.+ “Chititsani kuti masana, mthunzi wanu uphimbe malo aakulu ndiponso uchititse mdima ngati wa usiku.+ Bisani anthu obalalika.+ Musaulule aliyense amene akuthawa.+
3 “Anthu inu, perekani malangizo. Chitani zimene zagamulidwa.+ “Chititsani kuti masana, mthunzi wanu uphimbe malo aakulu ndiponso uchititse mdima ngati wa usiku.+ Bisani anthu obalalika.+ Musaulule aliyense amene akuthawa.+