Obadiya 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwe sunayenera kuima pamphambano kuti uzipha anthu ake amene anali kuthawa.+ Sunayenera kugwira anthu ake opulumuka ndi kuwapereka kwa adani awo pa tsiku limene anakumana ndi tsoka.+
14 Iwe sunayenera kuima pamphambano kuti uzipha anthu ake amene anali kuthawa.+ Sunayenera kugwira anthu ake opulumuka ndi kuwapereka kwa adani awo pa tsiku limene anakumana ndi tsoka.+