Yeremiya 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kalanga ine! Tsiku limeneli ndi lalikulu+ moti palibe lofanana nalo.+ Limeneli ndi tsiku la masautso kwa Yakobo.+ Koma adzapulumuka m’masautso amenewa.”
7 Kalanga ine! Tsiku limeneli ndi lalikulu+ moti palibe lofanana nalo.+ Limeneli ndi tsiku la masautso kwa Yakobo.+ Koma adzapulumuka m’masautso amenewa.”