Danieli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo. Luka 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+
5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo.
19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+