1 Samueli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno dzanja la Yehova+ linakhala lamphamvu kwambiri pa Aasidodi, kutanthauza mzinda wa Asidodi ndi madera ake ozungulira, ndipo anayamba kuwasautsa ndi kuwakantha ndi matenda a mudzi.*+
6 Ndiyeno dzanja la Yehova+ linakhala lamphamvu kwambiri pa Aasidodi, kutanthauza mzinda wa Asidodi ndi madera ake ozungulira, ndipo anayamba kuwasautsa ndi kuwakantha ndi matenda a mudzi.*+