5 Ndipo muyenera kupanga zifanizo za matenda anu a mudzi ndi zifanizo za mbewa zoyenda modumpha+ zimene zikuwononga dziko, ndipo mupereke ulemerero+ kwa Mulungu wa Isiraeli. Mukatero, mwina adzachepetsako mphamvu ya dzanja lake pa inu, mulungu wanu ndi dziko lanu.+