Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “‘Pa zamoyo zonse zokwawa padziko lapansi, zodetsedwa ndi izi:+ Mfuko, mbewa yoyenda modumpha+ ndi mtundu uliwonse wa buluzi.

  • 1 Samueli 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chiwerengero cha mbewa zoyenda modumpha zagolide chinali chofanana ndi mizinda yonse ya Afilisiti ya olamulira asanu ogwirizana, kuyambira mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri mpaka ku mudzi wopanda mpanda.

      Mwala waukulu umene anakhazikapo likasa la Yehova ndiwo mboni mpaka lero m’munda wa Yoswa, amene kwawo kunali ku Beti-semesi.

  • Yesaya 66:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Anthu amene akudzipatula ndi kudziyeretsa kuti apite kuminda+ n’kukaima kuseri kwa fano limene lili pakati pa mundawo, amene akudya nyama ya nkhumba+ ndi chinthu chonyansa, amene akudya ngakhale makoswe,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena