1 Mbiri 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+ Salimo 18:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Anthu akangomva mphekesera chabe zokhudza ine, adzandimvera.+Alendo adzabwera kwa ine akunthunthumira.+ Yesaya 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu am’patse Yehova ulemerero,+ ndipo anthu a m’zilumba anene za ulemerero wake.+
28 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+
44 Anthu akangomva mphekesera chabe zokhudza ine, adzandimvera.+Alendo adzabwera kwa ine akunthunthumira.+