Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+

  • 1 Samueli 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno dzanja la Yehova+ linakhala lamphamvu kwambiri pa Aasidodi, kutanthauza mzinda wa Asidodi ndi madera ake ozungulira, ndipo anayamba kuwasautsa ndi kuwakantha ndi matenda a mudzi.*+

  • 1 Samueli 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chotero anatumiza uthenga ndi kusonkhanitsa olamulira onse ogwirizana a Afilisiti, n’kuwauza kuti: “Chotsani likasa la Mulungu wa Isiraeli pakati pathu, libwerere kwawo kuti lisatiphe.” Ananena zimenezi chifukwa mumzinda wonsewo+ anthu anali kuopa kuti afa, pakuti dzanja la Mulungu woona linali kuwasautsa kumeneko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena