Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+

  • 1 Samueli 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako zimene zinachitika n’zakuti, atazungulira ndi likasalo n’kufika nalo kumeneko, dzanja la Yehova+ linasautsanso mzindawo ndi chisokonezo chachikulu kwambiri. Iye anayamba kukantha anthu onse a mumzindawo, osasiyapo aliyense moti onsewo anagwidwa ndi matenda a mudzi.+

  • 1 Samueli 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chotero anatumiza uthenga ndi kusonkhanitsa olamulira onse ogwirizana a Afilisiti, n’kuwauza kuti: “Chotsani likasa la Mulungu wa Isiraeli pakati pathu, libwerere kwawo kuti lisatiphe.” Ananena zimenezi chifukwa mumzinda wonsewo+ anthu anali kuopa kuti afa, pakuti dzanja la Mulungu woona linali kuwasautsa kumeneko.+

  • 1 Samueli 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chotero Afilisiti anagonjetsedwa ndipo sanabwerenso m’dziko la Isiraeli.+ Dzanja la Yehova linapitiriza kukankhira kutali Afilisiti masiku onse a moyo wa Samueli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena