1 Samueli 14:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+ 1 Mafumu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Bambo anu anaumitsa goli lathu. Tsopano inuyo mufewetse+ ntchito yowawa ya bambo anu ndi goli lawo lolemera+ limene anatisenzetsa, ndipo tidzakutumikirani.”+
52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+
4 “Bambo anu anaumitsa goli lathu. Tsopano inuyo mufewetse+ ntchito yowawa ya bambo anu ndi goli lawo lolemera+ limene anatisenzetsa, ndipo tidzakutumikirani.”+