Yobu 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi Mulungu angamumvere kulira kwakeZowawa zikamugwera?+ Salimo 18:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Adzafuula kupempha thandizo, koma sipadzapezeka wowapulumutsa,+Adzafuulira Yehova, koma sadzawayankha.+ Miyambo 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ineyo ndidzakusekani tsoka likadzakugwerani.+ Ndidzakunyozani zimene mumaopa zikadzabwera,+ Mika 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa nthawiyo adzafuulira Yehova kuti awathandize, koma sadzawayankha.+ Adzawabisira nkhope yake pa nthawi imeneyo+ chifukwa cha zoipa zimene anali kuchita.+
41 Adzafuula kupempha thandizo, koma sipadzapezeka wowapulumutsa,+Adzafuulira Yehova, koma sadzawayankha.+
4 Pa nthawiyo adzafuulira Yehova kuti awathandize, koma sadzawayankha.+ Adzawabisira nkhope yake pa nthawi imeneyo+ chifukwa cha zoipa zimene anali kuchita.+