Genesis 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako, malowo anawatcha Beteli.+ Koma dzina lakale la mzindawo linali Luzi.+ Genesis 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala wachikumbutso umene ndauimika panowu, udzakhala nyumba ya Mulungu.+ Pa chilichonse chimene mudzandipatsa, sindidzalephera kukubwezerani chakhumi chake.”+ 1 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chaka ndi chaka Samueli anali kuzungulira m’madera a Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa,+ ndipo anali kuweruza+ Isiraeli m’malo onsewa.
22 Mwala wachikumbutso umene ndauimika panowu, udzakhala nyumba ya Mulungu.+ Pa chilichonse chimene mudzandipatsa, sindidzalephera kukubwezerani chakhumi chake.”+
16 Chaka ndi chaka Samueli anali kuzungulira m’madera a Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa,+ ndipo anali kuweruza+ Isiraeli m’malo onsewa.