1 Samueli 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Samueli ananyamuka kuchoka ku Giligala kupita ku Gibeya wa ku Benjamini. Ndiyeno Sauli anayamba kuwerenga anthu amene anali nayebe limodzi, ndipo anapeza amuna pafupifupi 600.+
15 Kenako Samueli ananyamuka kuchoka ku Giligala kupita ku Gibeya wa ku Benjamini. Ndiyeno Sauli anayamba kuwerenga anthu amene anali nayebe limodzi, ndipo anapeza amuna pafupifupi 600.+