Oweruza 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni. Oweruza 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atamva zimenezi anatenga anthu ake ndi kuwagawa m’magulu atatu+ n’kubisalira anthuwo m’thengo. Poyang’ana, anaona anthu akutuluka mumzindawo, ndipo anawaukira n’kuwakantha. Miyambo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+
16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni.
43 Atamva zimenezi anatenga anthu ake ndi kuwagawa m’magulu atatu+ n’kubisalira anthuwo m’thengo. Poyang’ana, anaona anthu akutuluka mumzindawo, ndipo anawaukira n’kuwakantha.
6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+