Genesis 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo. Numeri 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Paja kale makolo athu anapita ku Iguputo,+ ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri.+ Aiguputowo anatizunza ife ndi makolo athu.+ Machitidwe 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu+ aja anamwalirira.+
6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo.
15 Paja kale makolo athu anapita ku Iguputo,+ ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri.+ Aiguputowo anatizunza ife ndi makolo athu.+