Genesis 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako, anayamba kukusa ziweto zake zonse, ndi kutenganso katundu wake yense amene anapeza+ ku Padana-ramu, n’kunyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani kwa bambo ake Isaki.+ Genesis 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitawachulukira kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Dziko lachilendo limene anali kukhalalo linali litawachepera chifukwa cha kuchuluka kwa ziweto zawo.+
18 Kenako, anayamba kukusa ziweto zake zonse, ndi kutenganso katundu wake yense amene anapeza+ ku Padana-ramu, n’kunyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani kwa bambo ake Isaki.+
7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitawachulukira kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Dziko lachilendo limene anali kukhalalo linali litawachepera chifukwa cha kuchuluka kwa ziweto zawo.+