1 Samueli 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+ Miyambo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ukafooka pa tsiku la masautso,+ mphamvu zako zidzakhala zochepa.
26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+