1 Samueli 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsiku lotsatira, Sauli+ anagawa anthuwo m’magulu atatu.+ Amenewa analowa pakati pa msasawo pa ulonda wa m’mawa.*+ Atatero, anayamba kukantha Aamoni+ kufikira dzuwa litatentha. Otsala anawabalalitsa moti sipanatsale anthu awiri ali limodzi.+
11 Tsiku lotsatira, Sauli+ anagawa anthuwo m’magulu atatu.+ Amenewa analowa pakati pa msasawo pa ulonda wa m’mawa.*+ Atatero, anayamba kukantha Aamoni+ kufikira dzuwa litatentha. Otsala anawabalalitsa moti sipanatsale anthu awiri ali limodzi.+