2 Samueli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli. Salimo 78:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Choncho anasankha Davide mtumiki wake,+Ndipo anamuchotsa kumakola a nkhosa.+
8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli.