1 Samueli 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Jese anatenga bulu, mkate, thumba lachikopa+ la vinyo ndi mwana wa mbuzi, ndipo anazitumiza kwa Sauli kudzera mwa Davide mwana wake.+ Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+ Miyambo 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+
20 Pamenepo Jese anatenga bulu, mkate, thumba lachikopa+ la vinyo ndi mwana wa mbuzi, ndipo anazitumiza kwa Sauli kudzera mwa Davide mwana wake.+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+