Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 10:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma anthu opanda pake+ anali kunena kuti: “Kodi ameneyu angatipulumutse bwanji?”+ Chotero anamunyoza,+ moti sanam’bweretsere mphatso iliyonse.+ Koma Sauli anangokhala chete.+

  • 2 Mbiri 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yehova anachititsa kuti ufumuwo ukhazikike m’manja mwake+ ndipo Ayuda onse anapitiriza kupereka+ mphatso kwa Yehosafati. Chotero iye anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero wochuluka.+

  • Miyambo 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mphatso ndiyo mwala wamtengo wapatali m’maso mwa mwiniwake wolemekezeka.+ Kulikonse kumene amapita zinthu zimamuyendera bwino.+

  • Miyambo 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena