Miyambo 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aliyense wosalankhulapo mawu ake ndi wodziwa zinthu,+ ndipo munthu wozindikira amakhala wofatsa.+ Agalatiya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kufatsa ndi kudziletsa.+ Palibe lamulo loletsa zinthu zoterezi.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+