Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako mfumukaziyo inapatsa+ mfumuyo golide wokwana matalente* 120,+ mafuta a basamu+ ochuluka zedi, ndi miyala yamtengo wapatali. Mafuta a basamu amene mfumukazi ya ku Sheba inapatsa Mfumu Solomo, anali ochuluka kwambiri moti sipanakhalenso mafuta ochuluka ngati amenewo.

  • 2 Mbiri 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yehova anachititsa kuti ufumuwo ukhazikike m’manja mwake+ ndipo Ayuda onse anapitiriza kupereka+ mphatso kwa Yehosafati. Chotero iye anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero wochuluka.+

  • Miyambo 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+

  • Mateyu 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano atalowa m’nyumbamo, anaona mwanayo ndi mayi ake Mariya. Choncho anagwada ndi kumuweramira. Kenako anamasula chuma chawo ndi kupereka kwa mwanayo mphatso za golide, lubani ndi mule.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena