1 Samueli 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma anthu opanda pake+ anali kunena kuti: “Kodi ameneyu angatipulumutse bwanji?”+ Chotero anamunyoza,+ moti sanam’bweretsere mphatso iliyonse.+ Koma Sauli anangokhala chete.+ 1 Mafumu 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense anali kubweretsa mphatso+ chaka chilichonse+ monga zinthu zasiliva,+ zinthu zagolide, zovala, zida zankhondo,+ mafuta a basamu, mahatchi, ndi nyulu.+
27 Koma anthu opanda pake+ anali kunena kuti: “Kodi ameneyu angatipulumutse bwanji?”+ Chotero anamunyoza,+ moti sanam’bweretsere mphatso iliyonse.+ Koma Sauli anangokhala chete.+
25 Aliyense anali kubweretsa mphatso+ chaka chilichonse+ monga zinthu zasiliva,+ zinthu zagolide, zovala, zida zankhondo,+ mafuta a basamu, mahatchi, ndi nyulu.+