2 Mbiri 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aliyense anali kubweretsa mphatso+ chaka chilichonse monga zinthu zasiliva, zinthu zagolide,+ zovala,+ zida zankhondo, mafuta a basamu, mahatchi, ndi nyulu.*+
24 Aliyense anali kubweretsa mphatso+ chaka chilichonse monga zinthu zasiliva, zinthu zagolide,+ zovala,+ zida zankhondo, mafuta a basamu, mahatchi, ndi nyulu.*+