Salimo 68:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha kachisi wanu yemwe ali ku Yerusalemu,+Mafumu adzabweretsa mphatso kwa inu.+ Miyambo 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+
16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+