Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano panali munthu wina wopanda pake+ dzina lake Sheba,+ mwana wamwamuna wa Bikiri, wafuko la Benjamini. Iye analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi kunena kuti: “Tilibe gawo mwa Davide, ndipo tilibe cholowa mwa mwana wa Jese.+ Aisiraeli inu, aliyense apite kwa milungu+ yake!”

  • 2 Mbiri 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo anthu osowa chochita+ ndi opanda pake+ anasonkhana kumbali yake. Pamapeto pake iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu+ mwana wa Solomo pamene Rehobowamuyo anali wamng’ono komanso wamantha,+ ndipo sanathe kulimbana nawo.

  • Nahumu 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Taonani mapazi a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino.+ Iye akulengeza za mtendere. Iwe Yuda, chita zikondwerero zako.+ Kwaniritsa zimene walonjeza+ chifukwa palibe munthu aliyense wopanda pake amene adzadutsa pakati pako.+ Munthu wopanda pakeyo adzaphedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena